Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

July 8-14

1 ATESALONIKA 1-5

July 8-14
  • Nyimbo 90 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Pitilizani Kutonthozana ndi Kulimbikitsana”: (10 min.)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • 1 Ates. 4:3-6—Kodi munthu akacita dama, ‘amaphwanyila ufulu m’bale wake’ m’njila yanji? (it-1 863-864)

    • 1 Ates. 4:15-17—N’ndani amene adzatengedwa “m’mitambo kukakumana ndi Ambuye m’mlengalenga”? Nanga zimenezi zidzacitika bwanji? (w15 7/15 18-19 ¶14-15)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 1 Ates. 3:1-13 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 81

  • Apainiya Amalimbikitsa: (9 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Apainiya Amathandiza Kwambili. Pambuyo pake, yankhani mafunso aya: Kodi apainiya amalimbikitsa bwanji ena mu mpingo? Nanga imwe, apainiya a mu mpingo mwanu amakulimbikitsani bwanji?

  • Zitsanzo Zabwino Zimene Zimatilimbikitsa: (6 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Tifunika ‘Kuthamanga Mopilila’Tengelani Zitsanzo Zabwino. Ndiyeno, yankhani mafunso otsatila: Kodi mlongoyu anali na vuto lanji? Nanga anacita ciani kuti athandizike?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 74

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 100 na Pemphelo