Zatsopano pa JW.ORG

2026-09-15

NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA

Mawu a M’Baibulo​​—⁠“Lolani Kuti Mtendere wa Khristu Ulamulire Mʼmitima Yanu”

Kodi tingasonyeze bwanji kuti tikulola kuti “mtendere wa Khristu” uzilamulira m’mitima yathu?

2026-09-15

NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA

September 2026

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira wiki ya November 2–​December 6, 2026.

2026-09-15

MFUNDO ZA NSANJA YA OLONDA YOPHUNZIRA

December 2026

2026-09-08

NYIMBO ZATHU

Mwa Chikhulupiriro

Banja lina likuona mmene Yehova akuwathandizila kukhalabe ndi chiyembekezo komanso chikhulupiriro champhamvu ngakhale kuti akukhala ku dela komwe ndikosowa mtendere ndi zachuma.

2026-08-27

UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU–NDANDANDA YA MISONKHANO

September–October 2026

2026-08-24

NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA

Zinthu Zochititsa Chidwi za M’Baibulo​​—⁠Mtengo Umene Umadzuka M’mawa Kwambiri

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zinthu zochititsa chidwi zokhudza mtengo wa amondi komanso mmene Baibulo limaugwiritsira ntchito.

2026-08-24

NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA

Stéphane Landeroin: Mlengi Wanga Wamkulu Anachita Nane Chidwi

Werengani nkhaniyi kuti muone zomwe Stéphane ndi mkazi wake Claudine anaphunzirapo pa zomwe anakumana nazo pa nthawi yomwe ankachita umishonale, utumiki wa pa Beteli komanso utumiki woyang’anira dera.

2026-08-24

NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA

Mageti a Mzinda M’nthawi ya M’Baibulo

Kodi kale pamageti a mzinda pankachitika zotani?

2026-08-24

NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA

August 2026

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira October 5–​November 1, 2026.