Malo a Nkhani

 

NKHANI

Lipoti Lachiwiri la Bungwe Lolamulira la 2026

Mulipotili, timveketsa mmene tizionera nkhani yokhudza kugwiritsa ntchito magazi ako omwe posankha thandizo lachipatala komanso popangidwa opaleshoni.

NKHANI

Lipoti Lachiwiri la Bungwe Lolamulira la 2026

Mulipotili, timveketsa mmene tizionera nkhani yokhudza kugwiritsa ntchito magazi ako omwe posankha thandizo lachipatala komanso popangidwa opaleshoni.

Lipoti Loyamba la Bungwe Lolamulira la 2026

Mulipotili, tikambirana malangizo atsopano omwe angatithandize kuti tizichititsa maphunziro a Baibulo ogwira mtima pogwiritsa ntchito buku la Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale.

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 8 la 2025

Mulipotili, tiona mmene mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu akuthandizira anthu.

2025-12-16

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 7 la 2025

Mu lipotili, muli zinthu zosangalatsa zomwe zili mu Lipoti la Chaka cha Utumiki cha 2025 ndipo likufotokoza mmene Yehova wadalitsira ntchito yathu padziko lonse.

2025-10-01

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 6 la 2025

Mu lipotili tikambirana za lemba la chaka cha 2026 komanso nyimbo yatsopano.

2025-08-22

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 5 la 2025

Mu lipotili, tiona mfundo za m’Baibulo zomwe zingatithandize kusankha mwanzeru pa nkhani ya maphunziro owonjezera.

2025-07-08

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 4 la 2025

Mu lipotili, tikambirana mfundo za m’Baibulo zomwe zingatithandize kuti tizisankha zinthu mwanzeru pa nkhani ya zizindikiro komanso miyambo.

2025-05-27

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti Lachitatu la Bungwe Lolamulira la 2025

Mu lipoti lino tiona zimene tingachite pokonzekera kuchita zambiri potumikira Yehova m’miyezi ikubwerayi.

2025-03-24

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti Lachiwiri la Bungwe Lolamulira la 2025

Mu lipotili, tiona zimene gulu lathu lakhala likuchita pothandiza anthu kuti adziwe kulemba ndi kuwerenga komanso mtendere umene timapeza chifukwa cha nsembe ya dipo ya Yesu. Tionanso za kutulutsidwa kwa nyimbo yatsopano yomwe tidzaimbe pamsonkhano wa 2025.

2025-02-03

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti Loyamba la Bungwe Lolamulira la 2025

Mulipotili, tiona mmene tingagwiritsire ntchito gawo lakuti “Choonadi Chomwe Timakonda Kuphunzitsa Anthu,” lomwe lili mu zakumapeto A m’kabuku kakuti Muzikonda Anthu​—Muziwaphunzitsa. Kuphunzira mfundo za choonadizi kutithandiza kuti tizisangalala tikamakambirana ndi anthu mu utumiki.

2024-12-30

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 8 la 2024

Mulipotili, tikambirana zimene tingachite kuti tiziona moyenera abale ndi alongo amene amaoneka m’mavidiyo athu.

2024-11-28

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 7 la 2024

Mulipotili, timva zokhudza abale ndi alongo athu padziko lonse komanso tionera mbali yocheza ndi abale atsopano a m’Bungwe Lolamulira, omwe ndi M’bale Jody Jedele ndiponso Jacob Rumph.

2024-09-30

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 6 la 2024

Mu lipotili, tiona zimene tingachite kuti tipitirize kuyambitsa maphunziro a Baibulo.

2024-08-02

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 5 la 2024

Mulipotili, tiona zimene tingachite kuti tizikhulupirira kwambiri kuti ndi Ufumu wa Mulungu wokha umene ungathetse mavuto onse amene anthufe tikukumana nawo.

2024-06-24

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 4 la 2024

Mu lipotili, tiona zimene abale ndi alongo athu amene ali m’ndende chifukwa cha zimene amakhulupirira akuchita kuti ‘apitirize kugonjetsa choipa pochita chabwino.’​—Aroma 12:21.