Nyimbo za Chikhristu

Mvetserani kapena pangani dawunilodi nyimbo za Chikhristu zomwe zimagwiritsidwa ntchito potamanda komanso kulambira Yehova Mulungu. Pakupezeka nyimbo za mawu, zoimbidwa ndi zipangizo zokhazokha komanso manotsi.

NYIMBO ZATHU

Mwa Chikhulupiriro

Banja lina likuona mmene Yehova akuwathandizila kukhalabe ndi chiyembekezo komanso chikhulupiriro champhamvu ngakhale kuti akukhala ku dela komwe ndikosowa mtendere ndi zachuma.