Kodi n’zotheka kukhala ndi moyo mpaka kalekale?

Kodi n’zotheka kukhala ndi moyo mpaka kalekale?

“Olungama adzalandira dziko lapansi, ndipo adzakhala mmenemo mpaka kalekale.”Salimo 37:29.

Baibulo limanena kuti m’tsogolo

Kuti mudziwe zambiri, pitani pa jw.org.