NKHANI ZOSIYANASIYANA

Kale Lathu

Chinenero Chamanja cha ku Malawi
Kale Lathu
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1011720/univ/art/1011720_univ_sqr_xl.jpg

Kale Lathu

Werengani nkhani zokhudza anthu komanso zinthu zosiyanasiyana zimene zakhala zikuchitika m’mbiri ya Mboni za Yehova.

Mbiri Mwachidule

Mbiri ya Gulu Lathu​—Misonkhano

Onani zokhudza mbiri ya misonkhano ikuluikulu imene a Mboni za Yehova amachita.

Mbiri ya Gulu Lathu​—Oyang’anira Madera

Oyang’anira madera masauzande ambiri amalimbikitsa a Mboni za Yehova padziko lonse lapansi. Onani mmene ntchitoyi inayambira komanso zimene mungachite powathandiza.

Mbiri ya Gulu Lathu​—Ntchito Yomanga

Onani chifukwa chake a Mboni za Yehova amagwira kwambiri ntchito yomanga padziko lonse.

Mbiri ya Gulu Lathu​—Kuphunzitsa Pogwiritsa Ntchito Mafilimu ndi Mavidiyo

Dziwani zambiri zokhudza mbiri ya mmene a Mboni za Yehova akhala akupangira mafilimu komanso mavidiyo kwa zaka zoposa 100.

Mbiri ya Gulu Lathu​—Mphatso ya Nyimbo, Mbali Yoyamba

Onani zokhudza mbiri ya nyimbo komanso kuimba, onaninso mmene zimathandizira a Mboni za Yehova pankhani ya kulambira.

Mbiri ya Gulu Lathu​—Mphatso ya Nyimbo, Mbali Yachiwiri

Onani mabuku a nyimbo osiyanasiyana amene a Mboni za Yehova akhala akugwiritsa ntchito polambira pa zaka 100 zapitazi.

1931 mpaka Masiku Ano

Bungwe Lolamulira Limateteza Mgwirizano Wathu​—Mbali Yoyamba

Kodi Bungwe Lolamulira limachita zotani kuti lipitirize kukondana kwambiri ndi abale apadziko lonse?

Bungwe Lolamulira Limateteza Mgwirizano Wathu​—Mbali Yachiwiri

Kodi Bungwe Lolamulira la Mboni za Yehova lakhala likuchita zotani pofuna kulimbikitsa mgwirizano padziko lonse?

Mbiri ya Gulu Lathu​—Tikulalikira ‘M’chilankhulo Chilichonse’

Dziwani zambiri zokhudza mmene a Mboni za Yehova amagwiritsira ntchito zipangizo zapamwamba potulutsa mabuku opulintidwa komanso apazipangizo zamakono m’zilankhulo zoposa 1,000.