Pulogalamu ya Msonkhano wa 2023 wakuti “Khalani Oleza Mtima”

Lachisanu

Pulogalamu ya Lachisanu yachokera palemba la 1 Akorinto 13:4​—“Chikondi n’choleza mtima.”

Loweruka

Pulogalamu ya Loweruka ikuchokera palemba la 1  Atesalonika 5:14​—“Khalani oleza mtima kwa onse.”

Lamlungu

Pulogalamu ya Lamlungu yachokera pa lemba la Yesaya 30:18​—‘Yehova akuyembekezera moleza mtima kuti akukomereni mtima.’

Mawu kwa Osonkhana

Mfundo zothandiza kwa omwe asonkhana.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

ZOKHUDZA IFEYO

Misonkhano Yapachaka ya Mboni za Yehova

Aliyense ndi wolandiridwa ku misonkhanoyi ndipo ndi yaulere.