Malo a Nkhani
Ikusonyeza 121 - 130 ya 130
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 4 la 2020
M’bale wina wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza mfundo zimene gulu lizitsatira posankha zochita pa nkhani yoyambiranso kuchita zinthu zina zokhudza kulambira.
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 3 la 2020
Tamvani zimene Yehova anachita powathandiza kuti amvetsere nkhani yapadera komanso kuti achite mwambo wa Chakudya Chamadzulo cha Ambuye.
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 2 la 2020
Onerani kuti mudziwe zimene gulu la Yehova likuchita potsogolera anthu ake panthawi ya mavuto komanso zimene abusa achikondi akuchita potisamalira.
Lipoti la Bungwe Lolamulira
Imvani zimene a Mboni za Yehova ku South Korea, Italy komanso ku United States akuchita polimbana ndi mliri umene wavuta kwambiri wa kolonavairasi.
Ikusonyeza 121 - 130 ya 130

