Mboni za Yehova Padziko Lonse

Tanzania

  • Mudzi wa Ngibao kufupi ndi mzinda wa Arusha, Tanzania-Akugawira kabuku kakuti  Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha kwa Amasai

Mfundo Zachidule—Tanzania

  • 68,153,000—Chiwerengero cha anthu
  • 23,789—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 423—Mipingo
  • Pa anthu 2,959 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi