Mfundo Zachidule—Sierra Leone
- 8,820,000—Chiwerengero cha anthu
- 2,803—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 44—Mipingo
- Pa anthu 3,313 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi


M’mphepete mwa Nyanja, mumzinda wa Freetown ku Sierra Leone—Akuitanira munthu wa m’dera lawo ku Nyumba ya Ufumu kuti akasonkhane nawo