Mboni za Yehova Padziko Lonse

Mozambique

  • Bairro dos Pescadores, pafupi ndi mzinda wa Maputo ku Mozambique​—Akugawira magazini a Nsanja ya Olonda

Mfundo Zachidule—Mozambique

  • 35,632,000—Chiwerengero cha anthu
  • 109,531—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 2,072—Mipingo
  • Pa anthu 345 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi