Mfundo Zachidule—Spain
- 49,316,000—Chiwerengero cha anthu
- 127,840—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 1,377—Mipingo
- Pa anthu 388 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

Barcelona, Spain—A Mboni m’derali amalalikira m’zinenero monga Chiarabu, Chikatalani, Chingelezi, Chifulenchi, Chisipanishi komanso Chiudu
Ku Agaete pa zilumba za Canary m’dziko la Spain—Akugawira kabuku kakuti Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu!