Mboni za Yehova Padziko Lonse

Dominican Republic

  • Mumzinda wa Samaná ku Dominican Republic—Akuonetsa vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo kwa munthu wogulitsa kokonati

Mfundo Zachidule—Dominican Republic

  • 11,520,000—Chiwerengero cha anthu
  • 39,936—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 532—Mipingo
  • Pa anthu 299 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi