Mboni za Yehova Padziko Lonse

Albania

  • Gjirokastër, Albania​—Akupatsa munthu wina kabuku ka m’Chingelezi kakuti Was Life Created?

Mfundo Zachidule—Albania

  • 2,363,000—Chiwerengero cha anthu
  • 5,349—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 77—Mipingo
  • Pa anthu 444 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi