Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani!

Magazini athu ofotokoza za m’Baibulo akupezeka m’zinenero zoposa 150 kuphatikizapo m’chinenero chamanja ndipo mungathe kuwakopera. Magazini ya Nsanja ya Olonda imatisonyeza kugwirizana kwa zinthu zomwe zikuchitika m’dzikoli ndi maulosi a m’Baibulo. Magaziniyi imalimbikitsa anthu ndi uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu komanso imalimbikitsa kuti anthu azikhulupirira Yesu Khristu. Magazini ya Galamukani! imatiuza mfundo zomwe zingatithandize kupirira mavuto a masiku ano ndiponso imatilimbikitsa kuti tizidalira lonjezo la Mlengi wathu lakuti tiziyembekezera dziko latsopano limene mudzakhala mtendere.

Sankhani chinenero chimene mukufuna pa kabokosi ka zinenero, kenako dinani kabatani ka Fufuzani kuti muone magazini amene alipo m’chinenerocho.

NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA

March 2026

Nkhaniyi tidzaiphunzira wiki ya May 4–​June 7, 2026.

GALAMUKANI!

Kodi Muyenera Kukhulupirira Kuti Kuli Mlengi?​—⁠Fufuzani

Onani mfundo zochititsa chidwi zokhudza mmene chilengedwe komanso moyo unayambira padzikoli.

ONANI

GALAMUKANI!

GALAMUKANI!

GALAMUKANI!

GALAMUKANI!

GALAMUKANI!

NSANJA YA OLONDA

NSANJA YA OLONDA

NSANJA YA OLONDA

NSANJA YA OLONDA

NSANJA YA OLONDA

NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA

NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA

NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA

NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA

NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA

NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA

NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA

NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA

NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA

MFUNDO ZA NSANJA YA OLONDA YOPHUNZIRA

MFUNDO ZA NSANJA YA OLONDA YOPHUNZIRA

MFUNDO ZA NSANJA YA OLONDA YOPHUNZIRA

MFUNDO ZA NSANJA YA OLONDA YOPHUNZIRA

MFUNDO ZA NSANJA YA OLONDA YOPHUNZIRA

MFUNDO ZA NSANJA YA OLONDA YOPHUNZIRA

MFUNDO ZA NSANJA YA OLONDA YOPHUNZIRA

MFUNDO ZA NSANJA YA OLONDA YOPHUNZIRA

MFUNDO ZA NSANJA YA OLONDA YOPHUNZIRA