Kukhala na Makhalidwe Abwino
Njila Yopezela Cimwemwe—Kukhutila Komanso Kupatsa
Ambili amaganiza kuti munthu amakhala wacimwemwe akapeza cuma cambili. Kodi kukhala na ndalama komanso katundu wambili kumabweletsa cimwemwe cokhalitsa? Kodi zocitika zimaonetsa ciani?
Kupatsa Kumapindulitsa
Kupatsa kumapindulitsa inu ndi ena. Kumalimbikitsa mgwilizano na ubwenzi. Mungacite ciani kuti muzipeleka mokondwela?
Njila Yopezela Cimwemwe—Cikondi
Kuonetsana cikondi n’kofunika kwambili kuti munthu akhale wacimwemwe.
Tsankho—Onetsani Cikondi
Kuonetsa cikondi kumathetsa tsankho. Ganizilani zimene mungacite.
Tsankho—Onetsani Cifundo
Kodi kusoŵa cifundo kungakhale cizindikilo ca ciani?
Kufatsa—Kumaonetsa Nzelu
Si capafupi kukhalabe wofatsa tikacitilidwa zinthu mopanda cilungamo, koma Baibo imalimbikitsa Akhiristu kukhala ofatsa. N’ciani cingakuthandizeni kukhala na khalidwe laumulungu limeneli?
Njila Yopezela Cimwemwe—Kukhululuka
Umoyo wokhala wokhumudwa na kusunga cakukhosi, si umoyo wacimwemwe ndipo umaononga thanzi.

