Cinyanja
Kuvutika Maganizo
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1011741/univ/wpub/1011741_univ_sqr_xl.jpg

Kuvutika Maganizo

Acinyamata ambili amakhala na vuto la kusungulumwa, nkhawa, kuvutika maganizo, komanso kutopa kwambili. Dziŵani zimene mungacite kuti musamavutike maganizo.

Zovutitsa Maganizo

Kulimbana ndi Bvuto la Kusungulumwa

Onani malangizo osabvuta amene angakuthandizeni kulimbana ndi bvuto la kusungulumwa kuti muzitha kumaceza ndi anthu ena.

Zovuta Zina

Kugonjetsa Munthu Amene Akukuvutitsani Popanda Kumenyana Naye

Dziŵani cifukwa cake anthu ena amavutitsa anzawo komanso mmene mungadzitetezele.