Kugonana
Kugonana pakokha si cinthu coipa, koma tifunika kulamulila cilakolako cathu ca kugonana. Kodi mungacite bwanji zimenezi popeza anthu ambili m’dzikoli amakonda zaciwelewele?

ACINYAMATA