ACINYAMATA

Banja

Cinyanja
Banja
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1011742/univ/wpub/1011742_univ_sqr_xl.jpg

Banja

Kodi zimakuvutani kugwilizana ndi makolo anu? Kodi simugwilizana kwenikweni ndi abale anu? Baibo ingakuthandizeni kuthana ndi mabvuto amenewa komanso mabvuto ena amene mungakumane nao m’banja.

Ubale Wanu na Makolo Anu

Ningakambe Nawo Bwanji Makolo Anga?

Kodi mungatani kuti mulankhulane ndi makolo anu pamene mukuona ngati simufuna kulankhula?

Ningakambilane Bwanji na Makolo Anga?

Malangizo aya angakuthandize kukambilana mosavuta na makolo ako.

Kodi Ningacite Ciani kuti Makolo Anga Anipatse Ufulu Wowonjezeleka?

Muona kuti mwakula ndipo makolo anu ayenela kucita namwe zinthu monga wamkulu, koma mwina iwo saona conco. Mungacite ciani kuti iwo ayambe kukudalilani?