Nchito Yathu Yofalitsa Mabuku
NCHITO YOFALITSA MABUKU
Zithunzi—Ana Amakonda Mavidiyo
Onankoni zimene ana ananena za mavidiyo ochuka ozikidwa pa Baibo akuti ‘Khalani Bwenzi la Yehova,’ a tikadoli ta Kalebe ndi Sofia.
NCHITO YOFALITSA MABUKU
Zithunzi—Ana Amakonda Mavidiyo
Onankoni zimene ana ananena za mavidiyo ochuka ozikidwa pa Baibo akuti ‘Khalani Bwenzi la Yehova,’ a tikadoli ta Kalebe ndi Sofia.
Mmene Zofalitsa Zathu Zimawafikila Anthu mu Congo
Mboni za Yehova zimayenda maulendo aatali kukapeleka ma Baibo na zofalitsa zophunzitsa Baibo kwa anthu m’dziko la Congo.