N’ciyani cimacitika pa Misonkhano Yathu Yacigawo? LIZANI N’ciyani cimacitika pa Misonkhano Yathu Yacigawo? Onani zimene mudzapeza mukapezeka pa msonkhano wacigawo wa Mboni za Yehova. Pepani, yakana kulila. Citani daunilodi Vidiyo Iyi Mungakondenso Izi ZOKHUDZA IFE Mukapezekepo pa Msonkhano wa 2026 wakuti: “Cimwemwe Camuyaya” Tikukupemphani kuti mukapezekepo pamsonkhano wacigao wa masiku atatu wa caka cino wa Mboni za Yehova.