N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? LIZANI N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? Tambani vidiyoyi kuti muone zimene zimacitika. Pepani, yakana kulila. Citani daunilodi Vidiyo Iyi Mungakondenso Izi MAVIDIYO OYAMBILAPO ULALIKI Kodi Mboni za Yehova ni Anthu Otani? Anthu ambili amafuna kudziŵa kuti Mboni za Yehova ni anthu otani. Fufuzani zokhudza iwo. MAFUNSO AMENE AMAFUNSIDWA KAŴILI-KAŴILI Kodi Phunzilo la Baibulo N’ciani? Pezani mayankho a mafunso okhudza mmene timacitila phunzilo la Baibulo laulele. MAFUNSO AMENE AMAFUNSIDWA KAŴILI-KAŴILI Kodi Ndalama Zoyendetsela Nchito ya Mboni za Yehova Zimacokela Kuti? Ŵelengani kuti mudziŵe cifukwa cake nchito yolalikila padziko lonse ikupita patsogolo kwambili ngakhale kuti sitiyendetsa mbale ya zopeleka ndi kupeleka cakhumi. ZOKHUDZA IFE MBONI Kapezekemponi pa Misonkhano ya Mboni za Yehova Fufuzani kumene timakumana komanso mmene timalambilila. Onse ni olandilidwa ndipo sipakhala kuyendetsa mbale ya zopeleka. Pulintani Gaŵilani Gaŵilani N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? MISONKHANO N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? Cinyanja N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/502014315/univ/art/502014315_univ_sqr_xl.jpg