Tengani nyimbo zauzimu zotsitsimula zoimba potamanda ndi polambila Yehova Mulungu. Pali nyimbo za mau ndi zamalimba.

Sankhani cinenelo pa kabokosi ka zinenelo, ndiyeno dinizani polemba kuti Funani kuti muone nyimbo ndiponso mitundu yake m’cineneloco.