Onani zimene zilipo

Magazini a Nsanja ya Mlonda ndi Galamuka!

Magazini athu ofotokoza Baibulo alipo m’zinenelo zopitilila 200, ndipo mungawatenge pa webusaiti imeneyi. Mungawatengenso a m’cinenelo ca manja. Nsanja ya Mlonda imafotokoza zocitika za padziko lapansi malinga ndi ulosi wa m’Baibulo. Imatonthoza anthu ndi uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu, ndipo imawalimbikitsa kukhulupilila Yesu Kristu. Galamuka! imafotokoza mmene tingapililile mavuto masiku ano. Imathandizanso anthu kukhulupilila lonjezo la Mlengi lakuti m’dziko latsopano mudzakhala mtendele ndi cisungiko.

Sankhani cinenelo pa kabokosi ka zinenelo, ndiyeno dinizani polemba kuti Funani kuti muone zofalitsa ndiponso mitundu yake m’cineneloco.

 

ONANI

GALAMUKA!

GALAMUKA!

GALAMUKA!

GALAMUKA!

GALAMUKA!

NSANJA YA MLONDA

NSANJA YA MLONDA

NSANJA YA MLONDA

NSANJA YA MLONDA

NSANJA YA MLONDA

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA