Phunzilani kwa Mabwenzi a Yehova—Zocita
Gwilitsani nchito zocita izi kupanga zithunzi za m’mavidiyo akuti Phunzilani kwa Mabwenzi a Yehova, ndipo kambilanani maphunzilo ofunika ndi ana anu.
Mefiboseti
Mungacite ciani kuti mukhalebe acimwemwe mukacitilidwa zopanda cilungamo monga anacitila Mefiboseti?
Yosefe
Mungaphunzile ciani kwa Yosefe amene anali mnzake wa Yehova?
Yoswa ndi Kalebe
Kodi mungaphunzile ciani kwa Yoswa ndi Kalebe amene anali mabwenzi a Yehova?
Abigayeli
Mungaphunzile ciyani kwa Abigayeli amene anali bwenzi la Yehova?
Debora
Kodi mungaphunzile kwa Debora amene anali bwenzi la Yehova
Pepani, palibe mawu olingana amene mwasankha.

