Ufumu wa Mulungu Unayamba Kulamulila mu 1914
Onani mmene ulosi wa m’Baibo umaonetsela kuti 1914 ni caka cimene Ufumu wa Mulungu unayamba kulamulila kumwamba, ndiponso caka cimene “masiku otsiliza” anayamba.—2 Timoteyo 3:1.

ZIPHUNZITSO ZOFUNIKA ZA M’BAIBO