Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

LAIBULALE YA JW

Mmene Mungaigwiritsire Ntchito pa Windows 8 Kapena pa Windows Phone 8

Mmene Mungaigwiritsire Ntchito pa Windows 8 Kapena pa Windows Phone 8

Laibulale ya JW ndi pulogalamu yovomerezeka imene inapangidwa ndi a Mboni za Yehova. Pulogalamuyi ili ndi Mabaibulo osiyanasiyana komanso mabuku ndi timabuku tothandiza pophunzira Baibulo.