Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

LAIBULALE YA JW

Mmene Mungaigwiritsire Ntchito pa Zipangizo za Android

Laibulale ya JW ndi pulogalamu yovomerezeka imene inapangidwa ndi a Mboni za Yehova. Pulogalamuyi ili ndi Mabaibulo osiyanasiyana komanso mabuku ndi timabuku tothandiza pophunzira Baibulo.

 

 

Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri

Kodi mitundu yosiyanasiyana yomwe ili pa m’ndandanda wa mabuku a m’Baibulo ikuimira chiyani?

N’chifukwa chiyani Baibulo la Kingdom Interlinear silioneka pa chipangizo changa cha Android?