Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

PULOGALAMU YOPHUNZIRIRA CHINENERO YA PA JW

Mmene Mungaigwiritsire Ntchito pa iPad, iPhone ndi iPod touch

Mmene Mungaigwiritsire Ntchito pa iPad, iPhone ndi iPod touch

Pulogalamu yophunzirira chinenero ya pa JW inakonzedwa ndi a Mboni za Yehova kuti izithandiza anthu amene akuphunzira chinenero kuti azidziwa mawu ambiri a chinenerocho komanso mmene angachilankhulire muutumiki komanso m’misonkhano.