Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

JW LANGUAGE

Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri Okhudza JW Language (Pa Zipangizo za Android)

Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri Okhudza JW Language (Pa Zipangizo za Android)

Pulogalamu Yophunzirira Chinenero ya pa JW imagwira ntchito pa zipangizo izi:

  • Matabuleti komanso mafoni a Android (okhala ndi pulogalamu ya 4.1 kapena ena a posachedwapa)

Zinthu zina zomwe zingakuthandizeni kugwiritsa ntchito pulogalamu imeneyi ziyamba kupezeka posachedwapa:

  • Matabuleti a Kindle Fire

Panopa tilibe maganizo odzakhala ndi zinthu zothandiza pogwiritsa ntchito zipangizo zotsatirazi:

  • Matabuleti komanso mafoni a Android omwe amagwiritsa ntchito pulogalamu ya 4.0 kapena ena omwe anatuluka m’mbuyomu

 

Munthu wina amene amadziwa bwino kugwiritsa ntchito Pulogalamu Yophunzirira Chinenero ya pa JW akhoza kukuthandizani. Ngati palibe, lembani fomu yokuthandizani kupeza mayankho ndipo kenako tumizani fomuyo.