Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

PULOGALAMU YOPHUNZIRIRA CHINENERO YA PA JW

Mmene Mungaigwiritsire Ntchito pa Zipangizo za Android

Mmene Mungaigwiritsire Ntchito pa Zipangizo za Android

Pulogalamu yophunzirira chinenero ya pa JW inakonzedwa ndi a Mboni za Yehova kuti izithandiza anthu amene akuphunzira chinenero kuti azidziwa mawu ambiri a chinenerocho komanso mmene angachilankhulire muutumiki komanso m’misonkhano.

 

 

M'CHIGAWO ICHI

Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri Okhudza JW Language (Pa Zipangizo za Android)

Pezani mayankho a mafunso omwe anthu amafunsa kawirikawiri.