Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZOKUTHANDIZANI POPHUNZIRA

KODI BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI?

Kodi Zoona Zenizeni za Mulungu N’zotani?—Gawo 1

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mmene Mulungu amamvera, zinthu zoipa zikamatichitikira. Sindikizani tsamba lino ndipo muyankhe mafunso.

Yesetsani Kuti Muzilambira Mulungu M’njira Yovomerezeka (Gawo 2)

Kodi mungafotokozere bwanji ena mosamala zimene mumakhulupirira komanso kulemekeza maganizo awo?

Dipo la Yesu Ndi Mphatso ya Mulungu Yamtengo Wapatali Kuposa Zonse (Gawo 1)

Kodi n’zotheka kudzapulumuka chifukwa cha chochita zimene timakhulupirira?

Zimene Mungachite Kuti Mulungu Apitirize Kukukondani (Gawo 1)

Kodi mungatani kuti ubwenzi wanu ndi Yehova ukhale wabwino. Zokuthandizani pophunzirazi zingakuthandizeni kuganizira mofatsa zimene mumakhulupirira komanso kudziwa mmene mungafotokozere kwa anthu ena zomwe mumakhulupirirazo.