Zokuthandizani pophunzirazi zachokera m’mutu 16 wa buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?

Kodi Mulungu amavomereza kugwiritsa ntchito zifaniziro pomulambira? Nanga bwanji kukondwerera masiku obadwa komanso maholide achipembedzo? Onani zimene Baibulo limanena.