Zokuthandizani pophunzirazi zachokera m’mutu 17 wa buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?

Kodi Mulungu amayankhadi mapemphero athu? Ngati amayankha, amawayankha bwanji?