N’chifukwa chiyani munthu oyambirira Adamu anafa? Kodi ndi cholinga cha Mulungu kuti anthu azifa? Fufuzani zimene Baibulo limanena. Sindikizani nkhaniyi kenako muyankhe mafunsowo.