Zokuthandizani pophunzirazi zachokera m’mutu 19 wa buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?

N’chiyani chingakuthandizeni kuyandikira Mulungu pambuyo pophunzira zokhudza Iyeyo? Mungatani kuti musasiye kukonda Mulungu?