Onani zomwe Baibulo limaphunzitsa zokhudza zimene zingathandize atumiki a Mulungu kuti akhalebe okhulupirika ngakhale atayesedwa.