Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZOKUTHANDIZANI POPHUNZIRA

KODI BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI KWENIKWENI?(ZOKUTHANDIZANI POPHUNZIRA)

Muziona Moyo Ngati Mmene Mulungu Amauonera (Gawo 2)

Mfundozi zachokera m’mutu 13 wa buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?

Onani zimene Baibulo limaphunzitsa pa nkhani yogwiritsa ntchito magazi molakwika. Komanso onani njira imodzi yokha yoyenera kugwiritsa ntchito magazi yomwe ingapulumutse moyo wathu.

Pemphero Lingakuthandizeni Kukhala pa Ubwenzi ndi Mulungu (Gawo 2)

Onani zimene Baibulo limanena pa nkhani yokhudza mmene tiyenera kupempherera komanso nthawi yoyenera kupemphera.

Zimene Mungachite Kuti Banja Lanu Lizisangalala (Gawo 2)

Kodi makolo ndiponso ana angaphunzirepo chiyani pa chitsanzo cha Yesu? Ganizirani zimene mumakhulupirira komanso zimene Baibulo limanena.

Ubatizo Umatithandiza Kuti Tikhale pa Ubwenzi ndi Mulungu (Gawo 3)

Kodi Mkhristu amene wadzipereka kwa Mulungu ayenera kutani? Nanga N’chifukwa chiyani anthu amene amakondadi Mulungu ayenera kutsimikiza kuti azichita zinthu mogwirizana ndi kudziperekako pamoyo wawo?