Kodi Baibulo limanena kuti pali zinthu zina zabwino zimene zizichitika ‘m’masiku otsiriza’ ano? Kodi ndi zinthu zabwino ziti zimene zidzachitike masiku otsiriza akadzatha? Taonani

zimene Baibulo limanena pa nkhaniyi.