Kodi Ufumu wa Mulungu unachita kale zinthu ziti? Nanga kodi udzachita zotani m’tsogolo? Werengani kuti mudziwe zimene Baibulo limanena pankhaniyi.