Pitani ku nkhani yake

BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI

Kodi Munthu Akafa Amapita Kuti? (Gawo 1)

Werengani mfundo zolondola zopezeka m’Baibulo zokhudza anthu amene anamwalira.

Sindikizani nkhaniyi kenako muyankhe mafunso.

Pemphero Lingakuthandizeni Kukhala pa Ubwenzi ndi Mulungu (Gawo 3)

Baibulo limatiphunzitsa kuti Mulungu amayankha mapemphero athu m’njira zosiyanasiyana. Kodi angayankhe liti mapemphero anu nanga angawayankhe bwanji?

Zimene Mungachite Kuti Mulungu Apitirize Kukukondani (Gawo 2)

Mukadziwa choonadi chokhudza Mulungu iye adzakuthandizani kuti musasiye kumukonda komanso kuti mupitirize kumuyandikira

Yesetsani Kuti Muzilambira Mulungu M’njira Yovomerezeka (Gawo 2)

Kodi mungafotokozere bwanji ena mosamala zimene mumakhulupirira komanso kulemekeza maganizo awo?