Pitani ku nkhani yake

KODI BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI?

Kodi Mulungu Ali Nalo Cholinga Chotani Dziko Lapansili? (Gawo 1)

Werengani nkhaniyi kuti muone mmene zinthu zaipira masiku ano m’dzikoli, zomwe ndi zosiyana ndi zimene Mulungu anakonza poyambirira. Koperani nkhaniyi kenako muyankhe mafunsowo.

Pemphero Lingakuthandizeni Kukhala pa Ubwenzi ndi Mulungu (Gawo 3)

Baibulo limatiphunzitsa kuti Mulungu amayankha mapemphero athu m’njira zosiyanasiyana. Kodi angayankhe liti mapemphero anu nanga angawayankhe bwanji?

Zimene Mungachite Kuti Mulungu Apitirize Kukukondani (Gawo 2)

Mukadziwa choonadi chokhudza Mulungu iye adzakuthandizani kuti musasiye kumukonda komanso kuti mupitirize kumuyandikira

Yesetsani Kuti Muzilambira Mulungu M’njira Yovomerezeka (Gawo 2)

Kodi mungafotokozere bwanji ena mosamala zimene mumakhulupirira komanso kulemekeza maganizo awo?