Fufuzani kuti mudziwe amene akulamulira dzikoli, yemwe ndi amenenso akuchititsa kuti padzikoli pakhale mavuto. Sindikizani tsamba lino ndipo muyankhe mafunsowo.