Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZOKUTHANDIZANI POPHUNZIRA

BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI

Baibulo ndi Buku Lochokera kwa Mulungu (Gawo 2)

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe chifukwa chake Baibulo ndi lothandiza komanso lodalirika. Sindikizani tsamba lino ndipo muyankhe mafunso.

Zimene Mungachite Kuti Banja Lanu Lizisangalala (Gawo 2)

Kodi makolo ndiponso ana angaphunzirepo chiyani pa chitsanzo cha Yesu? Ganizirani zimene mumakhulupirira komanso zimene Baibulo limanena.

Ubatizo Umatithandiza Kuti Tikhale pa Ubwenzi ndi Mulungu (Gawo 3)

Kodi Mkhristu amene wadzipereka kwa Mulungu ayenera kutani? Nanga N’chifukwa chiyani anthu amene amakondadi Mulungu ayenera kutsimikiza kuti azichita zinthu mogwirizana ndi kudziperekako pamoyo wawo?

Zimene Mungachite Kuti Banja Lanu Lizisangalala (Gawo 1)

Kodi chofunika kwambiri n’chiyani kuti banja likhale losangalala? Ganizirani mofatsa zimene mumakhulupirira, onani zimene Baibulo limaphunzitsa, komanso onani mmene mungafotokozere zimene mumakhulupirira kwa anthu ena pogwiritsa ntchito zoti muchitezi.