Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

KODI BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI KWENIKWENI? (ZOKUTHANDIZANI POPHUNZIRA)

KODI BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI KWENIKWENI?(ZOKUTHANDIZANI POPHUNZIRA)

Muziona Moyo Ngati Mmene Mulungu Amauonera (Gawo 2)

Mfundozi zachokera m’mutu 13 wa buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?

Onani zimene Baibulo limaphunzitsa pa nkhani yogwiritsa ntchito magazi molakwika. Komanso onani njira imodzi yokha yoyenera kugwiritsa ntchito magazi yomwe ingapulumutse moyo wathu.

Yesetsani Kuti Muzilambira Mulungu M’njira Yovomerezeka (Gawo 1)

Kodi Mulungu amavomereza kukondwerera tsiku lobadwa, maholide a chipembedzo, komanso kugwiritsa ntchito zifaniziro pomulambira? Kodi Baibulo limati chiyani?

Kulambira Kumene Mulungu Amavomereza (Gawo 1)

Kodi zipembedzo zonse zimasangalatsa Mulungu? Ngati si zonse, kodi mungatani kuti mudziwe chipembedzo choona? Fufuzani zimene Baibulo limaphunzitsa ndipo onaninso zimene mumakhulupirira.

Khalani ndi Makhalidwe Amene Mulungu Amasangalala Nawo (Gawo 2)

Kodi n’zotheka kusangalatsa Mulungu ngakhale kuti Satana amatiyesa?