Pitani ku nkhani yake

Kodi Zamoyo Zinachita Kusintha Kapena Zinalengedwa?

Kodi Moyo Unayamba Bwanji?

Zoona zake n’zakuti pali anthu ambiri ophunzira kuphatikizapo asayansi ena omwe amakayikira zoti zamoyo zinachita kusintha kuchokera ku zinthu zina.

Kodi Mukudziwa Mmene Mulungu Analengera Zinthu Zonsezi?

Kodi nkhani ya m’Baibulo yonena za mmene zinthu zinalengedwera imagwirizana ndi zimene Baibulo limanena?

Zimene Baibulo Limatiuza Zokhudza Mlengi

Kodi zomwe Baibulo limanena zimagwirizana ndi zimene asayansi apeza?

Kodi Mulungu Anasintha Zamoyo Zina Polenga Mitundu Inanso ya Zamoyo?

Baibulo silitsutsa zimene asayansi amanena zoti mitundu ya zamoyo imatulutsanso zamoyo zina zofanana ndi zamtundu womwewo.

Kodi Mwana Wasukulu Amvere Ziti?

Mwana wasukulu yemwe wakhala akuphunzitsidwa kuti zamoyo zinachita kulengedwa nthawi zambiri sadziwa zoti amvere.

Kodi Baibulo Limanena Zotani Zokhudza Chilengedwe?

Baibulo limafotokoza za masiku 6 amene Mulungu analenga zinthu. Kodi masiku amenewa anali a maola 24?

Achinyamata Ena Akufotokoza Zokhudza Kukhulupirira Kuti Kuli Mulungu

M’vidiyo ya maminitsi atatuyi, achinyamata akufotokoza chifukwa chake amakhulupirira kuti kuli Mulungu.

Zachilengedwe Zimatiphunzitsa za Ulemerero wa Mulungu

Kodi tsiku lililonse mumaona zinthu zachilengedwe zochuluka bwanji? Zachilengedwe zimatithandiza kudziwa kuti Mulungu amatikonda kwambiri komanso kuti ali ndi nzeru zopanda malire.

Pulaneti Lokhala ndi Zamoyo

Padzikoli sipakanakhala zamoyo zina zilizonse pakanapanda zinthu zosiyanasiyana zodabwitsa zimene zilipo. Kodi zinthuzi zinangokhalapo pa zokha kapena pali winawake amene anazikonza?

Chinthu Chodabwitsa

Kaboni ndi wofunika kwambiri kuti moyo upangike. Kodi kaboni n’chiyani ndipo n’chifukwa chiyani ndi wofunika kwambiri?

Maselo Athu Ali Ngati Laibulale

N’chifukwa chiyani asayansi ena anasiya kukhulupirira kuti zamoyo zinachita kusintha?

Kodi Zinthu Zinachita Kulengedwa?—Gawo 1: N’chifukwa Chiyani Ndimakhulupirira Kuti Kuli Mulungu?

Kodi mungakonde kuti muzifotokozera ena molimba mtima zimene mumakhulupirira zoti kuli Mulungu? Werengani nkhaniyi kuti mupeze mfundo zimene zingakuthandizeni kuyankha ngati munthu wina wakufunsani zimene mumakhulupirira.

Kodi Zinthu Zinachita Kulengedwa?—Gawo 3: N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kukhulupirira Kuti Zinthu Zinachita Kulengedwa?

Kodi munthu amafunika kudana ndi sayansi n’cholinga choti azikhulupirira zoti zinthu zinachita kulengedwa?

Kodi Baibulo Limagwirizana Ndi Zimene Asayansi Amanena Zoti Zamoyo Zinachita Kusintha Kuchokera ku Zinthu Zina?

Kodi zimene Baibulo limanena zoti zinthu zinachita kulengedwa, zimatsutsana ndi zimene asayansi amanena?

Kodi Baibulo Limanena Zotani Zokhudza Nyama Zotchedwa Madainaso?

Kodi zomwe limanena zimagwirizana ndi sayansi?