Pitani ku nkhani yake

Zizolowezi Komanso Makhalidwe Oipa

Makhalidwe a Munthu

Kodi N’zotheka Kusintha Zomwe Munazolowera?

Muzizolowera kuchita zinthu zabwino osati zoipa.

Kodi Ndingatani Kuti Ndisamagonje Poyesedwa?

Onani zinthu zitatu zimene zingakuthandizeni kuti musamagonje mukayesedwa.

Fodya, Mankhwala Osokoneza Bongo ndi Mowa

Mungatani Kuti Musayambe Kumwa Mowa Mopitirira Malire?

Mfundo 5 zimene zingakuthandizeni kuti musamamwe mowa mopitirira malire ngakhale pamene muli ndi nkhawa kwambiri.

Kodi Baibulo Limanena Kuti Kumwa Mowa Ndi Tchimo?

Baibulo limasonyeza kuti mowa ukhoza kuthandiza munthu amene akudwala m’mimba komanso likhoza kuthandiza munthu kuti azisangalala.

Kodi Ndiyenera Kudziwa Chiyani pa Nkhani Yomwa Mowa?

Onani mmene mungapewere kuphwanya malamulo, kuononga mbiri yanu, kuchitidwa nkhanza zokhudza kugonana, kukonda kwambiri mowa komanso imfa.

Kodi Mawu a Mulungu Amati Chiyani pa Nkhani ya Kusuta Fodya?

M’Baibulo mulibe mawu akuti fodya, ndiye tingadziwe bwanji zimene limanena pa nkhaniyi?

Kodi Kusuta Ndi Tchimo?

Popeza kuti m’Baibulo mulibemo nkhani yokhudza kusuta, ndiye zingatheke bwanji kuti liyankhe funso limeneli?

Khalidwe Langa Loipa Linanditopetsa

Dmitry Korshunov anali chidakwa, koma kenako anayamba kuwerenga Baibulo tsiku lililonse. Kodi n’chiyani chimene chinamuthandiza kuti asinthe khalidwe lake n’kukhala munthu wosangalala

Kufalitsa Nkhani Pazipangizo Zamakono

Musamagwiritse Ntchito Zipangizo Zamakono Monyanyira

Dzifunseni mafunso 4 kuti muone ngati mukugwiritsa ntchito zipangizo zamakono monyanyira.

Dzitetezeni Kuti Musamapusitsidwe ndi Nkhani Zabodza

Nkhani zolakwika, malipoti abodza ndi nkhani zamphekesera zafala kwambiri ndipo zingakubweretsereni mavuto.

Kodi Ndiyenera Kudziwa Zotani Zokhudza Kusewera Magemu a Pazipangizo Zamakono?

Mwina simunaganizirepo ubwino komanso kuipa kosewera magemu.

Kodi Zipangizo Zanu Zimakulamulirani Kapena Mumazilamulira?

Masiku ano anthu ambiri akugwiritsa ntchito zipangizo zamakono, koma musamalole kuti zimenezi zizilamulira moyo wanu. Nanga mungadziwe bwanji kuti mwayamba kukonda kwambiri zipangizo zanu? Ngati mulidi ndi vuto limeneli kodi mungatani kuti mulithetse?

Juga

Zimene Baibulo Limanena pa Nkhani ya Kutchova Juga

Kodi ndi masewera osangalatsa chabe?

Zolaula

Kodi Kuonera Zolaula Kuli Ndi Mavuto Otani?

Kodi kuonera zolaula kumakhudza bwanji anthu komanso mabanja?

Kodi Baibulo Limaletsa Kuonera Zolaula?

Ngati mukufuna kusangalatsa Mulungu, werengani nkhaniyi kuti mudziwe mmene Mulungu amaonera nkhani yoonera zolaula.

N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kupewa Kuonerera Zolaula?

Kodi kuonera zolaula n’kofanana motani ndi kusuta fodya?

Kodi Mukulephera Kusiya Kuonerera Zinthu Zolaula?

Baibulo lingakuthandizeni kuti mumvetse cholinga cha zinthu zolaula.

Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani ya Zolaula Ndiponso Kukambirana Zokhudza Kugonana pa Intaneti?

Masiku ano, mavidiyo, mabuku, nyimbo ngakhalenso zithunzi zolaula zachuluka kwambiri. Kodi zimenezi zilibe vuto lililonse?