Pitani ku nkhani yake

Ntchito Komanso Ndalama

Ntchito Yolembedwa

Mavuto a M’dzikoli​—Muzisamala Ndalama

Mukamagwiritsa ntchito bwino ndalama, sizingadzakuvuteni mukadzakumana ndi mavuto.

Kodi Kugwira Ntchito Mwakhama Ndi Kwachikale?

Anthu ambiri safuna kugwira ntchito zina chifukwa amaziona kuti ndi zonyozeka. Koma anthu ena amagwira ntchito mwakhama ndipo zimenezi zimachititsa kuti azisangalala. Kodi n’chiyani chimawathandiza kuti azisangalala ndi ntchito yawo?

Mfundo za M’Baibulo Zomwe Zingakuthandizeni Ngati Mwachotsedwa Ntchito

Phunzirani njira zokwanira 6 zomwe zingakuthandizeni.

Zimene Baibulo Limanena pa Nkhani ya Ntchito

Kodi mungasankhe bwanji ntchito?

Kodi Mungatani Ngati Mukupanikizika Chifukwa cha Ntchito?

Zinthu 4 zimene zingakuthandizeni kuti musamapanikizike chifukwa cha ntchito.

Kodi Inuyo Mumatanganidwa Kwambiri?

Anthu ambiri zimawavuta kuti azikwanitsa kugwira bwino ntchito yawo komanso kusamalira mabanja awo. Kodi n’chiyani chimachititsa zimenezi? Nanga tingatani kuti tithane ndi vutoli?

Nkhani za Ndalama

Kodi Ndalama ndi Zimene Zimabweretsa Mavuto Onse?

Zimene anthu ambiri amakonda kunena zoti “ndalama ndi muzu wa zoipa zonse,” zimangosonyeza kuti samvetsa zimene Baibulo limafotokoza.

Kugwiritsa Ntchito Bwino Ndalama

Kodi mfundo za m’Baibulo zingakuthandizeni bwanji kupewa mavuto a zachuma?

Zimene Baibulo Limanena pa Nkhani ya Ndalama

Kodi ndalama ndi zimene zimabweretsa mavuto onse?

Kodi Mungatani Kuti Musakhale Wokonda Ndalama?

M’nkhaniyi muli mafunso 7 amene angakuthandizeni kuti mudzifufuze ngati ndalama mumaziona m’njira yoyenera.

Mungatani Kuti Muzikhala Wosangalala​—Kukhala Wokhutira Komanso Wopatsa

Ambiri amaona kuti munthu amene ali ndi chuma kaya katundu wambiri ndi amene amakhala wosangalala. Koma kodi munthu akakhala ndi ndalama komanso katundu amakhala wosangalala nthawi zonse? Kodi ochita kafukufuku anapeza zotani pa nkhaniyi?

Kodi Maphunziro Ndi Ndalama Zingatithandize Kukhala Ndi Tsogolo Labwino?

Anthu ambiri aona kuti maphunziro akuyunivesite ndiponso chuma sizinawathandize kupeza zomwe ankayembekezera.

N’chifukwa Chiyani Anthu Amakonda Kugula Katundu Wambirimbiri?

N’chifukwa chiyani anthu ambiri amakonda kugula zinthu ngakhale zimene sakufunikira? Kodi mungatani kuti otsatsa malonda asakukopeni?

Kodi Mayiko Angathe Kuyendetsa Chuma Mokomera Aliyense?

Pali boma limene lingathe kulamulira dziko lapansi m’njira yabwino kwambiri, n’kuthetseratu umphawi ndi mavuto azachuma.

Zinthu Zitatu Zimene Sitingagule ndi Ndalama

Ndalama zimatithandiza kuti tigule zinthu zofunika pa moyo wathu koma zinthu zimene zingatipangitse kukhala ndi moyo wosangalala sizingagulidwe ndi ndalama.

Kuda Nkhawa Chifukwa cha Kusowa kwa Ndalama

Bambo wina anakwanitsa kusamalira banja lake ngakhale pamene mitengo ya zinthu inali itakwera kwambiri.

Ndinapeza Chuma Chenicheni

Kodi munthu yemwe bizinesi yake inkamuyendera kwambiri anapeza bwanji chuma chamtengo wapatali kuposa ndalama?

Kugwiritsa Ntchito Bwino Ndalama

Zimene Mungachite Ngati Mukupeza Ndalama Zochepa

Mavuto azachuma akabwera mwadzidzidzi zimadetsa nkhawa, koma mfundo za m’Baibulo zingakuthandizeni kuti muzitha kugwiritsa ntchito ndalama zochepa.

Kodi Baibulo Lingathandize pa Nkhani ya Mavuto Azachuma Ndiponso Ngongole?

Ndalama sizingakuthandizeni kukhala wosangalala koma pali mfundo za m’Baibulo zinayi zimene zingakuthandizeni pa mavuto azachuma.

Kodi Mungatani Kuti Musamawononge Ndalama Zambiri?

Musadikire mpaka ndalama zanu kutha musanayambe kuganizira njira yoyenera yogwiritsira ntchito ndalama. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene mungachite kuti muzigwiritsa ntchito ndalama mosamala.

Kodi Ndingatani Kuti Ndisamawononge Ndalama?

Kodi nthawi ina munapitapo mu shopu kuti mukangoona zinthu koma n’kugula chinthu chodula kwambiri? Ngati ndi choncho, nkhaniyi ikuthandizani.

Kodi Mukufuna Kubwereranso Kunyumba?

Kodi zinthu zakuvutani ndipo mukuona kuti mukufunikanso kubwerera kwanu? Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mfundo zomwe zingakuthandizeni kuti zinthu ziyambenso kukuyenderani bwino.

Kodi Ndibwerekedi Ndalama?

Mfundo za m’Baibulo zingakuthandizeni kudziwa zoyenera kuchita.

Kulimbana ndi Umphawi

Umphawi Komanso Vuto Losowa Pokhala Zidzatha

M’Baibulo muli mfundo zomwe zingathandize anthu omwe akukumana ndi mavuto azachuma kuti asamade nkhawa.

Zimene Baibulo Limanena pa Nkhani ya Umphawi

Kodi anthu osauka kwambiri angakhale osangalala?

Kodi Umphawi Udzatha Padziko Lonse?

Kodi ndani angathetsedi umphawi?

Kodi Mulungu Amathandiza Anthu Ovutika?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mmene Mulungu amathandizira osauka.

Kodi Osamukira Kudziko Lina Amakapezadi Zimene Akufuna?

Kodi mumaona kuti banja lanu likhoza kumasangalala ngati mutasamukira kudziko lina?