Pitani ku nkhani yake

Kupirira Mavuto Aakulu

Kuvutika

Zimene Baibulo Limanena pa Nkhani ya Mavuto

Kodi Mulungu amamva bwanji tikamavutika?

Kodi Mavuto Amene Timakumana Nawo Ndi Chilango Chochokera kwa Mulungu?

Kodi Mulungu amagwiritsa ntchito matenda kapena mavuto polanga anthu pa zolakwa zimene anachita?

Kodi N’chiyani Chingandithandize Ndikakumana ndi Mavuto?

Achinyamata akufotokoza zimene anachita atakumana ndi mavuto.

Tiziyembekezera Kuti Zinthu Zidzakhala Bwino M’tsogolo

N’chifukwa chiyani tinganene kuti malonjezo a m’Baibulo ndi osiyana ndi malonjezo komanso maganizo a anthu?

Kodi Uchigawenga Udzatha?

Mpaka nthawi imene zonse zochititsa mantha komanso zachiwawa zidzathe, zinthu ziwiri zimene Baibulo limatilimbikitsa kuchita zingathandize anthu omwe akhudzidwa ndi zauchigawenga.

Kodi Ndiyenera Kudziwa Zotani Zokhudza Nkhanza za Kugonana?​—Gawo 2: Zimene Mungachite Ngati Munachitidwapo Nkhanza Zotere

Werengani zimene zinathandiza anthu omwe anachitidwa nkhanza zokhudza kugonana kuti azikhala osangalala.

Kodi Mulungu Amamva Chisoni Tikamavutika?

Anthu ena akaona mavuto omwe akuchitika padzikoli, amakayikira zoti Mulungu alipo. Werengani m’Mawu a Mulungu kuti mudziwe mmene Iye amamvera akaona anthu akuvutika.

N’chifukwa Chiyani Mulungu Walola Zinthu Zoipa Komanso Kuti Anthu Azivutika?

Kodi zinthu zoipa zinayamba bwanji, ndipo n’chifukwa chiyani Mulungu walola kuti zoipazo zipitirirebe mpaka pano? Kodi mavuto amenewa adzatha?

N’chifukwa Chiyani Mulungu Amalola Kuti Anthu Azivutika?

Anthu ambiri amafuna kudziwa kuti n’chifukwa chiyani padzikoli pali mavuto ambiri. Baibulo limapereka yankho logwira mtima pa nkhaniyi.

N’chifukwa Chiyani Mulungu Analola Kuti Anthu Ambirimbiri Aphedwe mu Ulamuliro wa Nazi ku Germany?

Anthu ambiri amafunsa chifukwa chake Mulungu yemwe ndi wachikondi amalola kuti anthu azivutika. Baibulo limapereka mayankho omveka bwino

Mavuto Onsewa Atha Posachedwapa

Mulungu walonjeza kuti adzachotsa zinthu zonse zomwe zimabweretsa mavuto. Kodi adzachita bwanji zimenezi ndipo adzazichita liti?

Imfa ya Munthu Amene Mumamukonda

Zimene Mungachite Mukaferedwa

Muone zinthu zimene zingakuthandizeni kupirira.

Kodi Mungatani Mutakumana Ndi Vuto Lalikulu?​—Munthu wa M’banja Lanu Akamwalira

Zaka 16 zapitazo, anthu 5 a m’banja la Ronaldo anamwalira pa ngozi ya galimoto. Ngakhale kuti imfayi imamupwetekabe, panopa ali ndi mtendere wa mumtima.

Zimene Zingakuthandizeni Mukaferedwa​—Zimene Mungachite Panopa

Anthu amene okondedwa awo anamwalira anaona kuti pali njira zingapo zomwe zinawathandiza kuti azisangalala.

Kodi Pangakhalenso Chifukwa Chokhalira Ndi Moyo Munthu Amene Timamukonda Akamwalira?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zinthu 5 zimene mungachite kuti muthe kupirira imfa ya munthu amene munkamukonda.

Mungatani Ngati Muli ndi Chisoni Chifukwa cha Imfa ya Bambo Kapena Mayi Anu?

Zimakhala zothetsa nzeru kwambiri bambo kapena mayi ako akamwalira. Kodi wachinyamata amene bambo kapena mayi anamwalira, angatani ngati ali ndi chisoni chifukwa cha imfa ya kholo lakelo?

Zimene Zimachitika Ana Akakhala ndi Chisoni

Kodi mfundo za m’Baibulo zinathandiza bwanji achinyamata atatu omwe makolo awo anamwalira kuti athe kupirira?

Kodi Mungayankhe Bwanji Mwana Wanu Atakufunsani za Imfa?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zinthu 4 zimene mungachite pothandiza mwana wanu kudziwa zokhudza imfa komanso mmene mungamuthandizire kupirira wachibale akamwalira.

Tingatsimikize Bwanji Kuti Amene Anamwalira Adzakhalanso Ndi Moyo?

Baibulo limapereka zifukwa ziwiri zokhulupirira kuti akufa adzakhalanso ndi moyo.

Kodi Pali Chiyembekezo Chotani Chokhudza Anthu Amene Anamwalira?

Kodi chimachitika n’chiyani munthu akamwalira? Kodi abale athu amene anamwalira tidzawaonanso?

Mfundo Zofunika Kwambiri Kwa Anthu Omwe Aferedwa

Baibulo limapereka malangizo othandiza kwambiri kwa anthu omwe aferedwa.

Ngozi Zadzidzidzi

Kodi Baibulo Lingakuthandizeni Pakachitika Ngozi Zam’chilengedwe?

Malangizo a m’Baibulo angakuthandizeni pasanachitike ngozi zam’chilengedwe, pamene zikuchitika komanso pambuyo pake.

Zimene Tingachite Kuti Tipulumuke Pakachitika Ngozi Zadzidzidzi

Kutsatira mfundozi kungapulumutse inuyo ndi anthu ena.

Kodi Pangakhalenso Chifukwa Chokhalira Ndi Moyo Ngati Pachitika Ngozi Zogwa Mwadzidzidzi?

M’Baibulo muli malangizo amene angakuthandizeni kupirira mukakumana ndi ngozi zogwa mwadzidzidzi.

Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani ya Ngozi Zadzidzidzi?

Kodi ngozi zadzidzidzi ndi chilango chochokera kwa Mulungu? Kodi Mulungu amathandiza bwanji anthu amene akhudzidwa ndi ngozi zadzidzidzi?

Chikhulupiriro Chinathandiza Kwambiri Anthu Omwe Anakhudzidwa ndi Mvula Yamkuntho ku Philippines

Anthu opulumuka akufotokoza zimene zinachitika pa nthawi ya mvula yamkuntho ya Haiyan.