Nkhaniyi yachokera mu vidiyo yakuti Ankalemekeza Kwambiri Baibulo ndipo ikufotokoza mmene William Tyndale anamasulirira Chipangano Chatsopano m’chingelezi.